Danieli 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa nthawi imeneyo, ndinapitirizabe kuyangʼana chifukwa ndinkamva mawu odzitukumula* amene nyanga ija inkalankhula.+ Ndinapitiriza kuyangʼana mpaka pamene chilombocho chinaphedwa ndipo thupi lake linaponyedwa pamoto nʼkuwonongedwa. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:11 Ulosi wa Danieli, tsa. 145
11 Pa nthawi imeneyo, ndinapitirizabe kuyangʼana chifukwa ndinkamva mawu odzitukumula* amene nyanga ija inkalankhula.+ Ndinapitiriza kuyangʼana mpaka pamene chilombocho chinaphedwa ndipo thupi lake linaponyedwa pamoto nʼkuwonongedwa.