Danieli 7:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ufumu, ulamuliro, ndi ulemerero wa maufumu apadziko lonse lapansi zinaperekedwa kwa anthu amene ndi oyera a Mulungu Wamkulu.+ Ufumu wawo udzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo maulamuliro onse adzawatumikira ndi kuwamvera.’ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:27 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2022, tsa. 14 Nsanja ya Olonda,1/15/2005, tsa. 162/1/1998, ptsa. 17-18 Ulosi wa Danieli, ptsa. 146-148
27 Ufumu, ulamuliro, ndi ulemerero wa maufumu apadziko lonse lapansi zinaperekedwa kwa anthu amene ndi oyera a Mulungu Wamkulu.+ Ufumu wawo udzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo maulamuliro onse adzawatumikira ndi kuwamvera.’
7:27 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2022, tsa. 14 Nsanja ya Olonda,1/15/2005, tsa. 162/1/1998, ptsa. 17-18 Ulosi wa Danieli, ptsa. 146-148