Danieli 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nditayangʼana ndinaona nkhosa yamphongo+ itaima pafupi ndi mtsinjewo ndipo inali ndi nyanga ziwiri.+ Nyanga ziwirizi zinali zazitali koma imodzi, imene inamera pomalizira, inali yaitali kuposa inzake.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:3 Ulosi wa Danieli, tsa. 166 Nsanja ya Olonda,3/15/1988, tsa. 27
3 Nditayangʼana ndinaona nkhosa yamphongo+ itaima pafupi ndi mtsinjewo ndipo inali ndi nyanga ziwiri.+ Nyanga ziwirizi zinali zazitali koma imodzi, imene inamera pomalizira, inali yaitali kuposa inzake.+