Danieli 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikupitiriza kuyangʼana, ndinaona mbuzi yamphongo+ ikuchokera kumadzulo* kudutsa padziko lonse lapansi koma sinkaponda pansi. Pakati pa maso a mbuziyo panali nyanga yoonekera patali.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:5 Ulosi wa Danieli, ptsa. 168-169 Nsanja ya Olonda,4/15/1988, ptsa. 22, 23-243/15/1988, tsa. 29
5 Ndikupitiriza kuyangʼana, ndinaona mbuzi yamphongo+ ikuchokera kumadzulo* kudutsa padziko lonse lapansi koma sinkaponda pansi. Pakati pa maso a mbuziyo panali nyanga yoonekera patali.+