-
Danieli 8:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Mbuziyo inkabwera kumene kunali nkhosa yamphongo ya nyanga ziwiri ija, imene ndinaiona itaima pafupi ndi mtsinje. Inkathamangira kumene kunali nkhosayo itakwiya kwambiri.
-