-
Danieli 8:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndinaona mbuziyo ikufika pafupi kwambiri ndi nkhosa yamphongoyo ndipo inakwiyira kwambiri nkhosayo. Kenako inagunda nkhosayo nʼkuthyola nyanga zake ziwiri, ndipo nkhosayo inalibe mphamvu zotha kulimbana nayo. Mbuziyo inagwetsera pansi nkhosayo nʼkuipondaponda ndipo panalibe woti aipulumutse ku mphamvu za* mbuziyo.
-