Danieli 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako mbuzi yamphongoyo inayamba kudzitukumula mopitirira muyezo. Koma itangokhala yamphamvu, nyanga yake yaikulu inathyoledwa. Pamene panali nyangayo panamera nyanga 4 zoonekera patali ndipo zinaloza kumphepo 4 zakumwamba.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:8 ‘Dziko Lokoma’, tsa. 26 Ulosi wa Danieli, tsa. 169 Nsanja ya Olonda,4/15/1988, ptsa. 24-25
8 Kenako mbuzi yamphongoyo inayamba kudzitukumula mopitirira muyezo. Koma itangokhala yamphamvu, nyanga yake yaikulu inathyoledwa. Pamene panali nyangayo panamera nyanga 4 zoonekera patali ndipo zinaloza kumphepo 4 zakumwamba.+