Danieli 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Imodzi mwa nyanga zimenezi inatulutsa nyanga ina yaingʼono ndipo mphamvu zake zinachuluka kwambiri moti zinafika kumʼmwera, kumʼmawa* ndi ku Dziko Lokongola.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:9 Nsanja ya Olonda,9/1/2007, tsa. 20 Ulosi wa Danieli, ptsa. 170, 171-173
9 Imodzi mwa nyanga zimenezi inatulutsa nyanga ina yaingʼono ndipo mphamvu zake zinachuluka kwambiri moti zinafika kumʼmwera, kumʼmawa* ndi ku Dziko Lokongola.+