-
Danieli 8:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiyeno ndinamva mngelo akulankhula ndipo mngelo wina anafunsa mngelo amene ankalankhulayo kuti: “Kodi masomphenya okhudza nsembe imene inkaperekedwa nthawi zonse komanso tchimo lobweretsa chiwonongeko apitiriza kuchitika kwa nthawi yaitali bwanji+ nʼkumachititsa kuti malo opatulika komanso gululo lizipondedwapondedwa?”
-