-
Danieli 8:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Iye anandiuza kuti: “Mpaka nsembe za tsiku ndi tsiku zokwana 2,300, zamadzulo ndi zamʼmawa, zitadutsa. Kenako malo opatulika adzakonzedwanso kuti akhale ngati mmene analili poyamba.”
-