-
Danieli 8:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndiyeno pamene ineyo Danieli ndinkaona masomphenyawo nʼkumawaganizira kuti ndiwamvetse, mwadzidzidzi ndinaona winawake wooneka ngati munthu ataima patsogolo panga.
-