Danieli 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako ndinamva mawu a munthu kuchokera pakati pa mtsinje wa Ulai.+ Iye anaitana kuti: “Gabirieli,+ munthuyo umuthandize kuti amvetsetse zimene waona.”+
16 Kenako ndinamva mawu a munthu kuchokera pakati pa mtsinje wa Ulai.+ Iye anaitana kuti: “Gabirieli,+ munthuyo umuthandize kuti amvetsetse zimene waona.”+