Danieli 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma akulankhula nane, ndinagona pansi chafufumimba nʼkugona tulo tofa nato. Ndiyeno iye anandigwira nʼkundiimiritsa pamalo omwe ndinaima aja.+
18 Koma akulankhula nane, ndinagona pansi chafufumimba nʼkugona tulo tofa nato. Ndiyeno iye anandigwira nʼkundiimiritsa pamalo omwe ndinaima aja.+