Danieli 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anandiuza kuti: “Ine ndikudziwitsa zimene zidzachitike kumapeto kwa nthawi yopereka chiweruzo, chifukwa masomphenyawo adzakwaniritsidwa pa nthawi yoikidwiratu yamapeto.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:19 Ulosi wa Danieli, tsa. 165 Nsanja ya Olonda,7/1/1987, tsa. 13
19 Kenako anandiuza kuti: “Ine ndikudziwitsa zimene zidzachitike kumapeto kwa nthawi yopereka chiweruzo, chifukwa masomphenyawo adzakwaniritsidwa pa nthawi yoikidwiratu yamapeto.+