Danieli 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mbuzi yamphongo yaubweya wambiri ikuimira mfumu ya Girisi,+ ndipo nyanga yaikulu imene inali pakati pa maso ake ikuimira mfumu yoyamba.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:21 Nsanja ya Olonda,6/15/2012, ptsa. 10-114/15/1988, ptsa. 22, 23-24 Ulosi wa Danieli, ptsa. 168-169
21 Mbuzi yamphongo yaubweya wambiri ikuimira mfumu ya Girisi,+ ndipo nyanga yaikulu imene inali pakati pa maso ake ikuimira mfumu yoyamba.+
8:21 Nsanja ya Olonda,6/15/2012, ptsa. 10-114/15/1988, ptsa. 22, 23-24 Ulosi wa Danieli, ptsa. 168-169