Danieli 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma inu Yehova, munakhala tcheru ndipo munatigwetsera tsoka chifukwa inu Yehova Mulungu wathu ndinu wolungama pa ntchito zonse zimene mwachita, koma ife sitinamvere mawu anu.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:14 Ulosi wa Danieli, tsa. 183
14 Koma inu Yehova, munakhala tcheru ndipo munatigwetsera tsoka chifukwa inu Yehova Mulungu wathu ndinu wolungama pa ntchito zonse zimene mwachita, koma ife sitinamvere mawu anu.+