Danieli 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndili mkati molankhula, kupemphera ndi kuvomereza machimo anga ndi machimo a anthu a mtundu wanga, Aisiraeli komanso kupempha Yehova Mulungu wanga kuti andikomere mtima pa nkhani yokhudza phiri loyera la Mulungu wanga,+
20 Ndili mkati molankhula, kupemphera ndi kuvomereza machimo anga ndi machimo a anthu a mtundu wanga, Aisiraeli komanso kupempha Yehova Mulungu wanga kuti andikomere mtima pa nkhani yokhudza phiri loyera la Mulungu wanga,+