-
Danieli 10:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Sindinadye chakudya chokoma, sindinadye nyama kapena kumwa vinyo ndipo sindinadzole mafuta aliwonse kwa milungu itatu yathunthu.
-