Danieli 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ine ndekha Danieli, ndi amene ndinaona masomphenyawo+ koma amuna amene ndinali nawo sanawaone. Komabe iwo anayamba kunjenjemera kwambiri ndipo anathawa nʼkukabisala.
7 Ine ndekha Danieli, ndi amene ndinaona masomphenyawo+ koma amuna amene ndinali nawo sanawaone. Komabe iwo anayamba kunjenjemera kwambiri ndipo anathawa nʼkukabisala.