Danieli 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho ndinatsala ndekha ndipo nditaona masomphenya odabwitsawa, mphamvu zonse zinandithera. Nkhope yanga imene inkaoneka yolemekezeka inasintha kwambiri, moti ndinalibenso mphamvu.+
8 Choncho ndinatsala ndekha ndipo nditaona masomphenya odabwitsawa, mphamvu zonse zinandithera. Nkhope yanga imene inkaoneka yolemekezeka inasintha kwambiri, moti ndinalibenso mphamvu.+