Danieli 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako ndinamva munthu uja akulankhula. Koma nditamva kuti akulankhula, ndinagona pansi chafufumimba nʼkugona tulo tofa nato.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:9 Ulosi wa Danieli, ptsa. 204-206
9 Kenako ndinamva munthu uja akulankhula. Koma nditamva kuti akulankhula, ndinagona pansi chafufumimba nʼkugona tulo tofa nato.+