Danieli 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno ndinamva dzanja likundikhudza+ ndipo linandigwedeza kuti ndidzuke. Nditadzuka ndinagwada nʼkugwira pansi ndi manja anga.
10 Ndiyeno ndinamva dzanja likundikhudza+ ndipo linandigwedeza kuti ndidzuke. Nditadzuka ndinagwada nʼkugwira pansi ndi manja anga.