16 Ndiyeno winawake wooneka ngati munthu anandiyandikira nʼkukhudza milomo yanga.+ Atatero, ndinayamba kulankhula ndipo ndinauza amene anali ataimirira patsogolo panga uja kuti: “Mbuyanga, ine ndikunjenjemera chifukwa cha zimene ndaona mʼmasomphenyawa ndipo mphamvu zandithera.+