Danieli 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Mʼchaka choyamba cha Dariyo+ Mmedi, ine ndinkamulimbikitsa ndipo ndinali ngati mpanda wolimba kwambiri kwa iye. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:1 Ulosi wa Danieli, tsa. 212
11 “Mʼchaka choyamba cha Dariyo+ Mmedi, ine ndinkamulimbikitsa ndipo ndinali ngati mpanda wolimba kwambiri kwa iye.