Danieli 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mfumu yakumʼmwera, imene ndi mmodzi mwa akalonga ake, idzakhala yamphamvu. Koma iye* adzaigonjetsa ndipo adzalamulira ndi mphamvu zazikulu kuposa za iyeyo.* Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:5 Ulosi wa Danieli, tsa. 218 Nsanja ya Olonda,7/1/1987, ptsa. 11-1210/15/1986, ptsa. 3-4
5 Mfumu yakumʼmwera, imene ndi mmodzi mwa akalonga ake, idzakhala yamphamvu. Koma iye* adzaigonjetsa ndipo adzalamulira ndi mphamvu zazikulu kuposa za iyeyo.*