Danieli 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye adzapita ku Iguputo ndi milungu yawo, zifaniziro zawo zachitsulo,* zinthu zawo zamtengo wapatali zasiliva ndi zagolide, pamodzi ndi anthu amene adzawagwire. Kwa zaka zingapo iye sadzalimbana ndi mfumu yakumpoto Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:8 Ulosi wa Danieli, ptsa. 220-221
8 Iye adzapita ku Iguputo ndi milungu yawo, zifaniziro zawo zachitsulo,* zinthu zawo zamtengo wapatali zasiliva ndi zagolide, pamodzi ndi anthu amene adzawagwire. Kwa zaka zingapo iye sadzalimbana ndi mfumu yakumpoto