-
Danieli 11:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ana ake adzakonzekera nkhondo ndipo adzasonkhanitsa gulu lalikulu la asilikali. Iye adzafika mwamphamvu kwambiri nʼkudutsa mwachangu mʼdzikolo ngati madzi osefukira. Koma adzabwerera, ndipo adzachita nkhondo mpaka kumzinda wake wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri.
-