Danieli 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno mfumu yakumʼmwera idzakwiya kwambiri ndipo idzapita kukamenyana ndi mfumu yakumpoto. Iye* adzakhala ndi gulu lalikulu, koma gululo lidzaperekedwa mʼmanja mwa mfumu inayo. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:11 Ulosi wa Danieli, tsa. 222
11 Ndiyeno mfumu yakumʼmwera idzakwiya kwambiri ndipo idzapita kukamenyana ndi mfumu yakumpoto. Iye* adzakhala ndi gulu lalikulu, koma gululo lidzaperekedwa mʼmanja mwa mfumu inayo.