Danieli 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Gululo lidzatengedwa ndipo iye* adzadzitukumula mumtima mwake moti adzachititsa kuti anthu masauzandemasauzande aphedwe. Iye adzakhala wamphamvu, koma sadzagwiritsa ntchito bwino mphamvu zakezo kuti zimuthandize. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:12 Ulosi wa Danieli, ptsa. 222-223
12 Gululo lidzatengedwa ndipo iye* adzadzitukumula mumtima mwake moti adzachititsa kuti anthu masauzandemasauzande aphedwe. Iye adzakhala wamphamvu, koma sadzagwiritsa ntchito bwino mphamvu zakezo kuti zimuthandize.