-
Danieli 11:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kenako mfumu yakumpoto idzabwerera kwawo nʼkusonkhanitsa gulu lalikulu kwambiri kuposa loyamba lija. Ndiyeno patapita nthawi yaitali, pambuyo pa zaka zingapo, mfumuyo idzabwera ndi gulu lalikulu la asilikali lokhala ndi zida zambiri.
-