Danieli 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mʼmasiku amenewo anthu ambiri adzaukira mfumu yakumʼmwera. Ndiyeno anthu achiwawa* pakati pa anthu a mtundu wako adzatengeka ndi zochitika zimenezi ndipo adzayesa kukwaniritsa masomphenya, koma adzapunthwa. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:14 Ulosi wa Danieli, ptsa. 223-224
14 Mʼmasiku amenewo anthu ambiri adzaukira mfumu yakumʼmwera. Ndiyeno anthu achiwawa* pakati pa anthu a mtundu wako adzatengeka ndi zochitika zimenezi ndipo adzayesa kukwaniritsa masomphenya, koma adzapunthwa.