-
Danieli 11:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Mfumuyo idzatsimikiza mtima kuti ifike ndi gulu lonse la asilikali a ufumu wake ndipo adzachita nayo mgwirizano moti idzakwaniritsa zolinga zake. Iyo idzaloledwa kuti iwononge mwana wamkazi. Mwana wamkaziyo zinthu sizidzamuyendera bwino ndipo sadzapitiriza kukhala wokhulupirika kwa mfumuyo.
-