-
Danieli 11:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Idzatembenukira kumadera amʼmbali mwa nyanja ndipo idzalanda madera ambiri. Koma mtsogoleri wa asilikali adzathetsa khalidwe lake lonyoza, moti iye sadzanyozedwanso. Mtsogoleriyu adzachititsa kuti kunyozako kubwerere kwa mfumuyo.
-