Danieli 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako idzabwerera* kumizinda yakwawo yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri. Kumeneko idzapunthwa nʼkugwa ndipo sidzakhalakonso. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:19 Ulosi wa Danieli, ptsa. 225-226, 231
19 Kenako idzabwerera* kumizinda yakwawo yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri. Kumeneko idzapunthwa nʼkugwa ndipo sidzakhalakonso.