Danieli 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Udindo wake udzatengedwa ndi wina amene adzachititse kuti wokhometsa msonkho* aziyendayenda mu ufumu waulemerero, koma mʼmasiku ochepa iye adzafa, osati chifukwa cha chiwawa kapena nkhondo. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:20 Ulosi wa Danieli, ptsa. 232-233, 249 Nsanja ya Olonda,12/15/1998, tsa. 77/1/1987, tsa. 12
20 Udindo wake udzatengedwa ndi wina amene adzachititse kuti wokhometsa msonkho* aziyendayenda mu ufumu waulemerero, koma mʼmasiku ochepa iye adzafa, osati chifukwa cha chiwawa kapena nkhondo.