Danieli 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye adzagonjetsa magulu a asilikali okhala ngati madzi osefukira ndipo adzawonongedwa. Mtsogoleri+ wa pangano nayenso adzawonongedwa.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:22 Ulosi wa Danieli, ptsa. 233, 236-238 Nsanja ya Olonda,12/15/1998, tsa. 77/1/1987, ptsa. 12-13
22 Iye adzagonjetsa magulu a asilikali okhala ngati madzi osefukira ndipo adzawonongedwa. Mtsogoleri+ wa pangano nayenso adzawonongedwa.+