-
Danieli 11:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndipo chifukwa cha mgwirizano umene adzapange naye, iye adzachita zinthu mwachinyengo nʼkukhala ndi mphamvu pogwiritsa ntchito mtundu waungʼono.
-