-
Danieli 11:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Pa nthawi yamtendere,* iye adzalowa mʼmadera abwino kwambiri achigawocho ndipo adzachita zinthu zimene ngakhale makolo ake ndi makolo a makolo ake sanachitepo. Adzagawira anthu zinthu zimene zawonongedwa, zimene zalandidwa komanso katundu wosiyanasiyana. Adzakonzera ziwembu malo okhala ndi mipanda yolimba kwambiri, koma kwa kanthawi kochepa.
-