-
Danieli 11:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Iye adzasonkhanitsa mphamvu zake ndi kulimbitsa mtima wake kuti aukire mfumu yakumʼmwera ali ndi gulu lalikulu la asilikali. Mfumu yakumʼmwera nayonso idzakonzekera nkhondo ndipo idzasonkhanitsa gulu la asilikali lalikulu kwambiri komanso lamphamvu. Koma iye* sadzapambana chifukwa adzamukonzera chiwembu.
-