Danieli 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anthu amene amadya zakudya zake zokoma ndi amene adzachititse kuti iye agonjetsedwe. Gulu lake la asilikali lidzagonjetsedwa* ndipo anthu ambiri adzaphedwa. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:26 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2020, tsa. 5 Ulosi wa Danieli, ptsa. 240, 241-242
26 Anthu amene amadya zakudya zake zokoma ndi amene adzachititse kuti iye agonjetsedwe. Gulu lake la asilikali lidzagonjetsedwa* ndipo anthu ambiri adzaphedwa.