Danieli 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mafumu awiri amenewa adzakhala ndi mtima wofuna kuchita zoipa ndipo adzakhala patebulo limodzi nʼkumauzana zabodza. Koma zolinga zawo zonse sizidzatheka chifukwa mapeto adzafika pa nthawi yake.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:27 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2020, tsa. 5 Ulosi wa Danieli, ptsa. 256-260 Nsanja ya Olonda,7/1/1987, tsa. 1310/15/1986, tsa. 5
27 Mafumu awiri amenewa adzakhala ndi mtima wofuna kuchita zoipa ndipo adzakhala patebulo limodzi nʼkumauzana zabodza. Koma zolinga zawo zonse sizidzatheka chifukwa mapeto adzafika pa nthawi yake.+
11:27 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2020, tsa. 5 Ulosi wa Danieli, ptsa. 256-260 Nsanja ya Olonda,7/1/1987, tsa. 1310/15/1986, tsa. 5