Danieli 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho iye* adzabwerera kudziko lakwawo ali ndi katundu wochuluka ndipo adzakhala ndi mtima wofunitsitsa kuukira pangano lopatulika. Iye adzakwaniritsa zolinga zake nʼkubwerera kwawo. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:28 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2020, tsa. 5 Ulosi wa Danieli, ptsa. 260-261
28 Choncho iye* adzabwerera kudziko lakwawo ali ndi katundu wochuluka ndipo adzakhala ndi mtima wofunitsitsa kuukira pangano lopatulika. Iye adzakwaniritsa zolinga zake nʼkubwerera kwawo.