-
Danieli 11:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Pa nthawi imene inaikidwiratu iye adzabweranso ndipo adzaukira mfumu yakumʼmwera. Koma sizidzakhala ngati mmene zinalili poyamba,
-