-
Danieli 11:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Anthu amene amachita zinthu zoipa zotsutsana ndi pangano adzawachititsa kuti ayambe mpatuko pogwiritsa ntchito mawu achinyengo. Koma anthu amene amadziwa Mulungu wawo adzapambana ndipo adzakwaniritsa zolinga zawo.
-