Danieli 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Anthu ozindikira+ pakati pa anthuwo adzathandiza anthu ambiri kuti amvetse zinthu. Kwa masiku angapo iwo adzapunthwa chifukwa cha lupanga, malawi a moto, kutengedwa ukapolo komanso chifukwa cha kuwonongedwa kwa zinthu zawo. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:33 Ulosi wa Danieli, ptsa. 272-273 Nsanja ya Olonda,11/1/1993, ptsa. 16-177/1/1987, tsa. 19
33 Anthu ozindikira+ pakati pa anthuwo adzathandiza anthu ambiri kuti amvetse zinthu. Kwa masiku angapo iwo adzapunthwa chifukwa cha lupanga, malawi a moto, kutengedwa ukapolo komanso chifukwa cha kuwonongedwa kwa zinthu zawo.