Danieli 11:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ena mwa anthu ozindikirawo adzapunthwa. Zidzakhala choncho kuti ntchito yoyenga ichitike chifukwa cha iwowo ndiponso kuti anthu ozindikira atsukidwe ndi kuyeretsedwa+ mpaka nthawi ya mapeto, chifukwa mapetowo adzafika pa nthawi yake. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:35 Ulosi wa Danieli, ptsa. 274-275 Nsanja ya Olonda,11/1/1993, ptsa. 17-18
35 Ena mwa anthu ozindikirawo adzapunthwa. Zidzakhala choncho kuti ntchito yoyenga ichitike chifukwa cha iwowo ndiponso kuti anthu ozindikira atsukidwe ndi kuyeretsedwa+ mpaka nthawi ya mapeto, chifukwa mapetowo adzafika pa nthawi yake.