-
Danieli 11:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Mfumu imeneyi sidzalemekeza Mulungu wa makolo ake. Sidzaganiziranso zofuna za akazi kapena za mulungu wina aliyense koma idzadzikweza pamwamba pa aliyense.
-