-
Danieli 11:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Idzapereka ulemu kwa mulungu amene amalemekezedwa mʼmalo okhala ndi mipanda yolimba kwambiri. Idzapereka ulemu kwa mulungu amene makolo ake sanamudziwe. Idzachita zimenezi popereka kwa mulunguyo golide, siliva, miyala yamtengo wapatali ndi zinthu zamtengo wapatali.
-