-
Danieli 11:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Mfumuyo idzakwaniritsa zolinga zake polimbana ndi malo otetezeka kwambiri okhala ndi mipanda yolimba kwambiri ndipo idzachita zimenezi pamodzi ndi* mulungu wachilendo. Onse amene ali kumbali yake idzawapatsa* ulemerero waukulu ndipo idzachititsa kuti anthu oterowo alamulire pakati pa anthu ambiri. Idzagawa malo kwa munthu aliyense amene adzalipire.
-