-
Danieli 11:43Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
43 Idzalamulira chuma chobisika cha golide ndi siliva komanso zinthu zonse zamtengo wapatali za Iguputo. Anthu a ku Libiya ndi a ku Itiyopiya adzamutsatira.
-